Mbiri ya Malaŵi - History of Malawi 1.5

3

Pro hodnocení programu se prosím nejprve přihlaste

Staženo
1 ×
(Chi-Chewa)

Dziko la Malaŵi lomwe kale linkatchulidwa kuti Nyasaland, ndi dziko la demokilase lomwe lili ndi anthu ambiri ndipo lili cha ku m’mwera kwa Africa. Dzikoli linayandikana ndi Zambia cha ku madzulo, Tanzania cha ku mpoto ndi Mozambique kuzungulira kum’mawa, kummwera ndi ku madzulo. Chiyambi cha dzina loti Malawi sichidziwika bwino bwino, koma anthu ofufuza amakhulupilira kuti dzinali linachokela kwa chilankhulo cha anthu a mu dzikoli a ku chigawo cha kummwera, ndipo limatanthauza “malawi a moto”, koma mbendela ya dzikoli limatanthauza "kwacha" kunena kuti dzuwa lawala mmamawa.

(English)

The History of Malawi covers the area of present-day Malawi. The region was once part of the Maravi Empire. In colonial times, the territory was ruled by the British, under whose control it was known first as British Central Africa and later Nyasaland. It became part of the Federation of Rhodesia and Nyasaland. The country achieved full independence, as Malawi, in 1964. After independence, Malawi was ruled as a one-party state under Hastings Banda until 1994.
  • Verze programu

    1.5

  • Poslední aktualizace od vývojáře

    27. 11. 2019

  • Počet stažení za měsíc

    0 ×

  • Velikost

    3,4 MB

  • Potřeba instalace:

    Ne

  • Web autora

    History1111

  • Podporované jazyky

    • Francouzština
    • ,
    • Němčina
Zobrazit více
Přejít do Google Play
Zdarma

Sdílet

TIP: Stahují se vám programy pomalu? Změřte si rychlost svého internetového připojení.